Mtsogoleri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering (ECG) Shepherd Bushiri wati ayamba kuthandiza mwana yemwe posachedwapa anaonesedwa m’masamba a nchezo akudyetsedwa dowe wa muwisi. Posachedwapa, anthu ambiri m’masamba a nchezo anagwidwa ndi chisoni kamba ka kanema yemwe anthu anamugawana kwambiri yemwe amaonetsa mwana wina wa zaka khumi ndi ziwiri (12) akudyetsedwa mondokwa wa muwisi. Malipoti […]
The post Bushiri athandiza mwana odyetsedwa dowe wamuwisi appeared first on Malawi 24.