Musadele nkhawa, tikonza vuto la Magetsi

Kampani yogulitsa magetsi m’dziko muno ya ESCOM yatsimikizira anthu okhala ku Majiga 2 ntauni ya Balaka kuti akhala atakonza vuto lomwe la magetsi pofika lolemba, pa 25 March, 2024. Izi zili mchikalata chomwe mkulu wa kampaniyi mu ma boma a Mangochi, Machinga, Ntcheu komanso Balaka, a Martin Mbwandira asainila pamodzi ndi m’modzi wa otsogolera nzikazi […]

The post Musadele nkhawa, tikonza vuto la Magetsi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください