Zosamvetsetseka! Bambo amangidwa popereka mimba kwa mwana wawo wa zaka 14

Apolisi mu mzinda wa Blantyre amanga mkulu wina yemwe dzina lake ndi Wonderful Itikani wa zaka 41, kamba komuganizira kuti wappereka mimba kwa mwana wake wa zaka 14. Malingana ndi Aaron Chilala Mneneri wa polisi ya Soche, Itikani akuganiziridwa kuti wakhala akuchita zogonana ndi mwana wakeyu kuchokera mchaka cha 2019 mpaka chaka chino. Chilala mkuluyu […]

The post Zosamvetsetseka! Bambo amangidwa popereka mimba kwa mwana wawo wa zaka 14 appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください