Pomwe akupitilira ndi ntchito yogawira chimanga anthu omwe akhudzidwa ndi njala m’dziko muno, mtsogoleri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering (ECG), Mneneri Shepherd Bushiri, wagawa chimanga kwa anthu opitilira 18,000 munzinda wa Lilongwe. Mneneri Bushiri wagawa chimangachi Lamulungu pa 17 March, 2024 kulikulu la ofesi yake ku Golden Peacock mu mzinda wa Lilongwe komwe khwimbi […]
The post Bushiri wagawa chimanga kwa anthu 18,000 ku Lilongwe appeared first on Malawi 24.