Khonsolo ya boma la Thyolo yapanga lamulo loti eni minda ikuluikulu ya tiyi adzipereka msonkho ku khonsoloyi. Wapampando wa khonsoloyi, Rhustin Banda, ndiye watsimikiza za nkhaniyi. A Banda ati kwa nthawi yaitali eni mindayi samalipira msonkho wa pa chaka ku khonsoloyi ngakhale amapanga phindu lochuluka chifukwa chosowa lamulo. “Minsonkhoyi ithandizira kupititsa pa tsogolo zitukuko za […]
The post Maesiteti ku Thyolo azipereka msonkho ku khonsolo appeared first on Malawi 24.