Anjatidwa kamba kogwililira mtsikana  wa zaka 14

Apolisi ku Chileka mu mzinda wa Blantyre amanga bambo Paul Mugawa a zaka 50 zakubadwa powaganizira kuti amagonana ndi mtsikana wa za 14. Mneneri wa apolisi ya Chileka, Jonathan Phillipo, wati a Mugawa anali pa ubwenzi ndi mtsinakayu kuyambila mwezi wa October chaka chatha. A Phillipo anati :”Mai a mwanayu ndiye anadzapereka lipoti ku polisi […]

The post Anjatidwa kamba kogwililira mtsikana  wa zaka 14 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください