A Manesi Justin, omwe ali ndi zaka 83 zakubadwa ndipo amachokera m’mudzi mwa Kwitanda, mfumu yaikulu Nsamala m’bomali m’mbuyomu, achikulire amakumana ndi zipsinjo zadzaoneni akapita kukalandira chithandizo cha mankhwala kuchipatala. Gogoyu adawonjezera kuti izi zidali chonchi kaamba kakuti ogwira ntchito za umoyo ena samawalabadira achikulirewa. Iwo ati tsopano achikulire okhala mozungulira zipatala za Kwitanda komanso […]
The post Achikulire ku Balaka ati tsopano akumalandira thandizo msanga ku chipatala appeared first on Malawi 24.