Pomwe akupitilira kuyendera zinthu zosiyanasiyana mchigawo cha ku mpoto, mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera, lero ali m’boma la Mzimba komwe akuyendera Tropha Estate ndipo akatelo apita ku Mzuzu kukayendera malo ophikira zinthu zosiyanasiyana a Kwithu Kitchen. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe boma latulutsa yofotokoza zomwe mtsogoleri wa dzikoyu achite lero pomwe akupitilira […]
The post Chakwera lero akuyendera Tropha Estate, Kwithu Kitchen appeared first on Malawi 24.