Ku nyumba ya malamulo kunabuka chipwirikiti masanawa, zomwe zidapangitsa kuti Kamlepo Kalua, phungu wa dera la ku mmawa m’boma la Rumphi komanso Christopher Manja phungu wa dera la ku m’mwera kwa boma la Salima atulusidwe mnyumbayi. Kalua anadzudzula boma lotsogozedwa ndi Tonse kuti silisamala chigawo chakumpoto pa ntchito zachitukuko ponena kuti boma lapereka ndalama zokwana […]
The post Kamlepo ayambitsa phokoso ku Parliament atadzudzula boma kuti sililabadira anthu aku mpoto appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.