Nkhondo siimanga mudzi: Tuno wapepesa Zani Challe

Potsatira kalata yomwe Zani Challe anatulutsa yodandaula komaso kuopseza kuti apanga chinthu china chomwe sananene pa Tuno kamba komunena kuti iye amagulitsa thupi komaso amachita malonda a mankhwala ozunguza ubongo, oyimbayu wapepesa tsopano. Nkhaniyi inayamba Lachiwiri usiku pomwe oyimba Tuno yemwe anabadwa Tunosiwe Mwakalinga amacheza mu pologalamu ya ‘Truth or Drink’ yomwe limapangitsa ndi gulu […]

The post Nkhondo siimanga mudzi: Tuno wapepesa Zani Challe appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください