Bwalo la milandu la Senior Resident Magistrate m’boma la Mangochi, lagamula anthu awiri omwe amabera anthu ndalama pomanama kuti mankhwala omwe amagulitsa amachiza matenda a AIDS kuti alipile chindapusa cha ndalama zokwana K2,450,000 aliyese. Posachedwapa, apolisi m’boma la Mangochi anamanga mayi Mary Saidi a zaka 25 komaso a Molly Kainga powaganizira kuti akhala akubera anthu […]
The post Obera anthu ponama kuti mankhwala awo amachiza AIDS agamulidwa chindapusa cha K4.9 miliyoni appeared first on Malawi 24.