Gulu la nzika zokhudzidwa ndi vuto la magetsi ku dera la Majiga 2 m’boma la Balaka lapeleka maola 24 ku kampani ya Escom kuti likonze vuto la magetsi lomwe akukumana nalo. Gululi kum’mawaku lidachita ziwonetsero pofuna kumema kampani yogawa komanso kugulitsa magetsiyi kuchita machawi pothana ndi vutoli. Anthu m’delari tsopano akhala opanda magetsi kuyambira pa […]
The post Nzika zauza Escom kuti ikonze magetsi pasanathe maola 24 appeared first on Malawi 24.