Bwalo la milandu ku Lilongwe lalamula a Arafat Goman kukakhala kundende kwa zaka 63 pa mlandu wakupha a Cecilia Lucy Kadzamira azaka 82 amene adali mchemwali wa a Tamandani Kadzamira, mthandizi wa mtsogoleri wakale wadziko lino a Dr Hastings Kamuzu Banda. Mkuluyu adazengedwa mlanduwu mchaka cha 2019 ndipo oweruza milandu a Zondi Mvula wati wapereka […]
The post Wagamulidwa kukakhala kundende zaka 63 appeared first on Malawi 24.