M’busa wa mpingo wa Bua African Abraham ali m’chitokosi cha apolisi ku Mchinji kaamba koganizilidwa kuti adaba mawaya amagetsi wa ndalama zokwana K297,000 a bungwe lopereka magetsi la Escom. Mneneri wa apolisi m’bomali watsimikiza zankhaniyi ndipo wati oganizilidwayu ndi a James Solomon a zaka 46 zakubadwa ndipo awagwira m’bandakucha wa lero pomwe iwo amasolola wayayu […]
The post M’busa wanjatidwa atagwidwa akuba mawaya amagetsi appeared first on Malawi 24.