UTM yati Chilima ndiye adzayimile Tonse Alliance mu 2025

Mlembi wamkulu wa chipani cha UTM Patricia Kaliati wati mtsogoleri wachipanchi a Saulos Chilima ndiwo adzayimile mgwirizano wa Tonse pa zisankho za mtsogoleri wa dziko lino mu 2025. Chipani cha UTM chati mgwirizano wawo ndi Malawi Congress Party (MCP) pa yemwe akudzaimira mgwirizano wa Tonse mu chisankho mu chikudzachi sudasinthe ndipo ‘udakali chimodzimodzi’. Mlembi wamkulu […]

The post UTM yati Chilima ndiye adzayimile Tonse Alliance mu 2025 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください