Zilikotu ziliko: Anthu m’masamba a nchezo akupitilirabe kung’ung’udza kamba kosamvetsa zomwe chiphona John Cena chinapanga Lamulungu lapitali pofika pa nsanja ya mwambo wina chitangobisa ulemelero wake ndi chikalata basi. Lamulungu lapitali pa 10 March, kunali mwambo opeleka mphatso kwa akatswiri osiyanasiyana omwe amautchula kuti Oscar Awards pa chingerezi ndipo mwambowu unachitikira ku malo otchedwa Dolby […]
The post John Cena afika pa nsanja ali chifupifupi bwamuswe appeared first on Malawi 24.