A Undule Mwakasungula omwe ndi m’modzi mwa anthu amene amayankhulapo pa ndale ati a Peter Mutharika akuyenera aganize bwino pa lingalilo lawo lofuna kudzapikisana nawo pa mpando wa upulezidenti. A Mwakasungula ati ngakhale a Mutharika akukhulupira kuti utsogoleri wawo ndi ofunikira, pali zolepheretsa zambiri kuti adzawineso pa chisankho cha 2025. “Zaka zawo, umunthu komaso nkhani […]
The post A Mutharika awapempha aganize bwino pa lingalilo lawo lofuna kuimanso appeared first on Malawi 24.