Anyamata awiri aswa mbiri lero mumpikisano wa Mzuzu City Half Marathon

Chikondi Mwanyali ndi amene wapambana masewera a Mzuzu City Half Marathon atathamanga mtunda otalika makilomita okwana 21 pa ola imodzi ndi mphindi zokwana zisanu ndi chimodzi. Mkulu wina amenenso wakonkhomola lekodi ndi Chancy Master pamene wakhala pa nambala yachiwiri atathamanga mtunda otalika makilomita okwana 21 pa ola limodzi ndi mphindi zokwana zisanu ndi ziwili. Chikondi […]

The post Anyamata awiri aswa mbiri lero mumpikisano wa Mzuzu City Half Marathon appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください