Chiopsezo cha Namondwe chachepelako, yatero Nthambi yoona zanyengo

Nthambi Yoona Zanyengo m’dziko muno yati chiyembekezo choti mpweya opepuka omwe uli mu nyanja ya mchere ya Indian Ocean usanduka namondwe chachepa. Nthambi yi yati namondweyo saakuyembekezekanso kubadwa m’masiku atatu akudzawa komabe mpweya opepukawu ukhala ukuyendabe panyanjayi koma ndizokayikitsa kuti ufika m’dziko lino. “Ngakhale izi zili chonchi, mpweyawu ulimbikitsa kugwa kwa mvula m’madera ambiri m’chigawo […]

The post Chiopsezo cha Namondwe chachepelako, yatero Nthambi yoona zanyengo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください