Oyimba amene sachita manyazi kuyika mimba yake pa mtunda pa masamba a mchezo, Avokado watulutsa nyimbo yatsopano yotchedwa ‘Msandipitilire’. Avocado yemwe dzina lake lenileni ndi Christopher Malera yemwenso amadziwika ndi dzina loti Amapiano Landlord waimba nyimboyi mothandizana ndi Ethel Kamwendo komanso Temwa. Avokado mokuwa ndi mawu ake okhakhala nyimbo kungoyamba amvekere ‘aya! ya! ya! ya! […]
The post Avocado watulutsa nyimbo yatsopano appeared first on Malawi 24.