Wapolisi azipha poziponya munsinje kamba ka chibwezi

  Wapolisi wina ku Rumphi wadziponya mu mtsinje wa South Rukulu omwe pano wadzadza ndikusefukira mbali zina m’bomali. Mneneri wa polisi mchigawo chakumpoto a Maurice Chapola, angotsimikiza zoti alandira lipoti lakusowa kwa a Ngamanya Mbale koma anakana kuyankhulapo zambiri ponena kuti kafukufuku wawo ali mkati. Koma yemwe watitsina khutu wati a Mbale adziponya mu mtsinjewu […]

The post Wapolisi azipha poziponya munsinje kamba ka chibwezi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください