Akatswiri pa nkhani za umoyo ati kuchepa kwa kapezedwe ka njira za kulera komaso kusiyila sukulu pa njira ndi zina zimene zikuonjezera chiwerengero cha atsikana omwe akubereka asanafike zaka 18. Mkulu wa za umoyo ndi achinyamata khonsolo ya Blantyre, Gift Kawalazila wati pafupipafupi atsikana 48 pa atsikana 100 aliwonse amene ali osapyola zaka 15 zakubadwa […]
The post Atsikana osakwana zaka 18 oposa 9800 anabereka ana ku Blantyre mu 2023 appeared first on Malawi 24.