Polojekiti yalimbikitsa uchembere ndi ubereki wabwino pakati pa achinyamata

Achinyamata okhala m’madera a mafumu akuluakulu Amidu komanso Kalembo m’boma la Balaka ati tsopano ali ndi mwayi opeza mauthenga osiyanasiyana okhudza uchembere komanso ubereki wabwino, zomwe akuti zapititsa kwambiri patsogolo miyoyo yawo komanso maphunziro awo.  Esnarth Taipi yemwe ndi wapampando wa gulu la achinyamata la Namanolo Youth club m’dera la mfumu yaikulu Amidu m’bomali wati   […]

The post Polojekiti yalimbikitsa uchembere ndi ubereki wabwino pakati pa achinyamata appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください