Aphungu akunyumba yamalamulo ati ndipofunika ndalama zamuthumba lachitukuko la Constituency Development Fund (CDF) zidzafike pafupifupi K1 billion kuti aphunguwa adzikwanitsa kupanga zitukuko zogwirika zomwe anthu am’madera awo amafuna. Wapampando wakomiti yanyumba yamalamulo yazosamalira anthu Sarvel Kafwafwa ndiyemwe wanena izi poyerekeza kuti maiko monga Zambia ndi Kenya thumbali lili ndi ndalama zochuluka mwakuti aphungu savutika kumapempha […]
The post Ngkhale CDF yakwezedwa kuchoka pa K100m kufika pa K200m, aphungu akufuna ikwelenso ifike pa K1 biliyoni appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.