Nduna yoona zachuma Simplex Chithyola- Banda watsindika kuti anthu amene amakhala m’matauni nawonso amakumana ndi umphawi wa dzaoneni. A Chithyola-Banda anena izi m’boma la Zomba pa mwambo okhazikitsa ndondomeko ya mtukula pakhomo wa m’mizinda ya Zomba, Blantyre, Lilongwe komanso Mzuzu. Malingana ndi ndunayi,ndi mtukula pakhomowu, umene ukuthandizidwa ndi a World Bank, mabanja okwana 105 000 […]
The post Chithyola akhazikisa ntchito yopereka ndalama kwa anthu ovutika okhala m’matauni: Anthu ayamba kulandira appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.