Chiwerengero cha anthu omwalira ndi ngozi ya madzi osefukira m’boma la Nkhotakota chakwera kufika pa 6 komanso ena anayi avulala. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe nthambi ya boma yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya DoDMA yatulutsa pa ngozi yomwe inachitika sabata latha. Anthu okwana 14,176 anakhudzidwa ndi ngoziyi pamene ena 9,378 akusungidwa pamene nyumba […]
The post Anthu 6 amwalira Kamba kamadzi osefukira ku Nkhota Kota, mabanja 17 176 akhuzidwa appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.