Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wauza Unduna wa Zamaphunziro kuti uwunikenso ndalama zomwe ophunzira mu sukulu za ukachenjede amalandira pamwezi kuti zikwezedwe. A Chakwera ati ophunzira mu sukulu za ukachenjede asamasowe zofunikira pa moyo wawo monga sopo, kuti aziika chidwi chawo chonse pa maphunziro. A Chakwera anena izi pa sukulu ya ukachenjede ya Malawi […]
The post Chakwera wauza unduna wa zamaphunziro kuti uwunikenso ndalama za ophunzira ku koleji amalandira appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.