Mutharika ayankhula ndi a Malawi Lachisanu lino

Lachisanu lino chidwi cha anthu chikhala ku Mangochi ku nyumba ya Page komwe mtsogoleli wa chipani cha Democratic Progressive (DPP), Professor Peter Mutharika, akhale akuyankhula ku mtundu wa a Malawi kudzera pa msonkhano wa atolankhani omwe achititse. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe chipani cha DPP chatulutsa momwe akudziwitsa anthu kuti a Mutharika achititsa nsonkhano […]

The post Mutharika ayankhula ndi a Malawi Lachisanu lino appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください