Wanjatwa pobera anthu kuti mankhwala ake amachiza AIDS

Apolisi m’boma la Mangochi, amanga mayi wa zaka 25 pomuganizira kuti wakhala akubera anthu ndalama pomawagulitsa mankhwala omwe amanama kuti amachiza matenda a HIV/AIDS. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Mangochi a Amina Tepani Daudi, mayi ochanuka m’masoyu ndi a Mary Julius omwe akuti akhala akusatsa mankhwala ajakiseni otchedwa Gammora kudzera pa tsamba lawo […]

The post Wanjatwa pobera anthu kuti mankhwala ake amachiza AIDS appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください