Chakwera akatsekulira chipatala cha khansa

Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera, lero akhala akutsekulira chipatala cha nthenda ya khansa mu nzinda wa Blantyre chomwe wamanga ndi mpondamatiki Thom Mpinganjira. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe boma latulutsa Lolemba yomwe wasainira ndi Colleen Zamba yemwe ndi mlembi wamkulu mu ofesi ya mtsogoleri ndi nduna zake (OPC). Malingana ndi kalatayi, a […]

The post Chakwera akatsekulira chipatala cha khansa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください