Tiyeni timenyebe nkhondo yolimbana mavuto a zachuma, watero Tobias

Mtsogoleri wa chipani cha Mzika Coalition, Milward Tobias, wapempha a Malawi kuti asatope pofuna kuthana ndi mavuto a zachuma omwe ali mu dziko muno. Izi zayankhulidwa pamene dziko lino likukumbukira amatiliti amene anamenyera ufulu kuti dziko lino kuti likhale loima palokha. Mu chikalata chomwe watulutsa, Mtsogoleriyu wati dziko lino likuyenera kukhala  ndi chidwi kwambiri pakumanga […]

The post Tiyeni timenyebe nkhondo yolimbana mavuto a zachuma, watero Tobias appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください