Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus McCarthy Chakwera wapempha Amalawi kuti achilimike pa ntchito yotukula madera awo posadalira kuti ena adzawagwirire ntchitoyo. Chakwera anena mauwa m’boma la Nkhata Bay Lamulungu pamwambo wokumbukira omwe adaphedwa ndi azungu pomenyera ufulu wa dziko lino. Iwo adati Amalawi ayenera kuphunzira kwa ‘makolo athu’ omwe adagwiritsa ntchito zipangizo zomwe zidalipo […]
The post Chakwera apempha Amalawi kuti achilimike pa ntchito yotukula dziko appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.
Moni Malawi 