Kunali kusinthana zibagera mkachisi wa Zolozolo CCAP yomwe uli pansi pa Livingstonia Synod ku Mzuzu kamba ka mkangano omwe unabuka pankhani wokhudza zachuma pakati pamamembala ndi akuluakulu ena ampingowu mpaka apolisi anathira utsi okhetsa misonzi kukhazikitsa bata. Nkhani yonse ikuti anthu omwe amayimba mkachisimu adawuzidwa kuti azipereka ndalama yokwana 35,000 akafuna kutenga nawo mbali. Koma […]
The post Munabuka ndewu mkachisi wa CCAP pankhani yokhudza zachuma appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 