Nthambi ya Immigration yatsutsa kuti maina a anthu omwe ali ndi ziphaso zoyendera asowa

Nthambi yoona zolowa ndi kutuluka mdziko muno ya DICS yati mphekesera zomwe zimkuveka kuti nthambiyi ilibe dzina ngakhale limodzi la anthu omwe ali ndi ziphaso zoyendera mdziko muno, ndizabodza. Nkhaniyi ikubwera pomwe nthambi ya DICS kufikira pano ikukanikabe kusindikiza ziphaso zoyendera kapena kugwira ntchito iliyose kamba ka akathyali ena omwe akuti anasokoneza sisitimu ya nthambiyi […]

The post Nthambi ya Immigration yatsutsa kuti maina a anthu omwe ali ndi ziphaso zoyendera asowa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください