Adzukulu okumba manda amangilira anthu awili pamtengo kumanda a Kabwabwa kamba kotolera chipepeso cha maliro popanda chilolezo kuchokera kwa amfumu a ku Area 25B (Kabwabwa) munzinda wa Lilongwe. Mayina a anthu awili omwe amangidwa pamtengowa ndi a Yusuf Steven komanso a Patrick Tambula. Nkhani yonse ikuti mderali munachitika zovuta ndipo anyamatawa anayamba kusonkhanitsa chipepeso popanda […]
The post Adzukulu amangilira njonda ziwili pamtengo ku manda a Kabwabwa appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
