Eli Njuchi walengeza kuti sakwanitsa kuyimba nawo pamapwando awiri azamayimbidwe omwe akhale akuchitika m’boma la Salima lero pa 1 March komanso mawa pa 2 March munzinda wa Blantyre kaamba kakuti sakupeza bwino. Katswiriyu wanena izi kudzera mumkalata yomwe iye watulutsa kudzera pa tsamba lake la mchezo la Fesibuku. Njuchi wati akupepesa kamba kakulephera kuyimba nawo […]
The post Eli Njuchi wati sakupeza bwino ndipo sakhala nawo kumapwando a lero appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
