Magetsi ayambiranso kuvuta m’boma la Mzimba

Magetsi ayambilanso kuvuta ku boma la Mzimba komwe anthu ayamba kukhalaso maola wochuluka kopanda magesi. Miyezi ingapo yapitayi, magetsi amavutanso zomwe zinapangitsa amabungwe komanso ochita malonda kudzuzula bungwe la ESCOM kamba kosalabadila kuwapatsa magezi. Mwezi watha, nduna yowona zamphamvu za magesi a Ibrahim Matola inakayendera ofesi ya Escom ya boma la Mzimba ndipo akuluakulu a […]

The post Magetsi ayambiranso kuvuta m’boma la Mzimba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください