Mtsogoleri wakale wa dziko lino, a Joyce Banda, apempha boma ndi mabungwe omwe akugawa chimanga kwa anthu omwe akhudzidwa ndi njala m’dziko muno kuti achite machawi kufikira madera ambiri anthu ambiri akhudzidwa ndi mavuto osowa chakudya. A Banda anayankhula izi ku Domasi boma la Zomba kumene anali nawo pa mwambo omwe bungwe la Shepperd Bushiri […]
The post Tisaleme kuthandiza anthu omwe akhudzidwa ndi njala – atero mai Joyce Banda appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 