Mayendedwe akhala ovutirapo pamene mlatho wapamtsinje wa Chitete omwe uli pafupi ndi sukulu ya sekondale yoyendera ya Boma Community Day Secondary school (C.D.S.S) mumanisipalite ya Kasungu wakokoloka ndi madzi kutsatira mvula yamphamvu yomwe yagwa kuyambira dzulo. Malipoti akuti mlathowu udayamba kukokoloka m’mwezi watha wa January ndipo mvula yomwe yakhala ikugwa mtauniyi yamalizitsa kambali komwe kadatsala. […]
The post Mlatho wakokoloka ndi madzi ku Kasungu appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 