Chidakwa chakana ngongole ya thobwa: Techno Brain ikuti sizikuyikhudza za kusokonekera kwa ntchito yopanga mapasipoti

Fisi anakana nsatsi: kampani ya Techno Brain yomwe ikuganizilidwa kuti ndi yomwe yasokoneza sisitimu ya nthambi yosindikiza ziphaso zoyendera mdziko muno yati iyo siyikukhudzidwa ndikusokonezedwa kwa sisitimuyi koma yati boma silikuyankhula kanthu paupangili omwe kampaniyi inapeleka pofuna kuthetsa vutoli. Nkhaniyi yayamba mwezi wa January pomwe manong’onong’ono akhala akumveka kuti nthambi ya “Immigration and Citizenship Services […]

The post Chidakwa chakana ngongole ya thobwa: Techno Brain ikuti sizikuyikhudza za kusokonekera kwa ntchito yopanga mapasipoti appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください