Bambo wina ku Dowa yemwe dzina lake ndi Kelvin Songazaudzu wa zaka 47 zakubadwa wadzimangilira kudenga la nyumba yake kaamba kamavuto a m’banja. Mneneri wa apolisi m’bomali a MacPatson Msadala watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati malemuwa ndi a m’mudzi wa Chimphapa m’dera la mfumu yayikulu Chakhaza ku Dowa komweko. Malingana ndi a Msadala, bamboyu wakhala […]
The post Bambo wina wadzikhweza ku Dowa appeared first on Malawi 24.