Amene akutsogolera zionetsero zotsutsana ndikusayenda bwino kwa zinthu m’dziko muno a Bon Kalindo, ati ngati boma siliyankha pempho lawo pa nkhani ya katoleledwe ka ndalama pa malo otolera ndalama ku magalimoto a Chingeni komanso Kalinyeke, iwo sabata yamawa atseka malo onsewa. A Kalindo omwe amayankhula pa msonkhano wa atolankhani Lachitatu ku Blantyre ati akufuna kuti […]
The post M’bindikiro ulipo pa Chingeni sabata ya mawa – Kalindo appeared first on Malawi 24.