Bungwe lowona za akatswili pa ukadaulo wa makina a ma kompyuta ndi zipangizo za makono la ICT- Association of Malawi (ICTAM) lati lili lokozeka kuthandiza ndi ukadaulo udziwi wawo ku bungwe lowona za anthu otuluka ndi kulowa m’dziko muno la Immigration pamene pakali pano likukumana ndi mavuto popanga ziphaso. Bungweli lati ilo monga bungwe lomwe […]
The post ICTAM yatasa dzanja pa bungwe la Immigration appeared first on Malawi 24.