Nyamata wazaka 19 wapha mzake polimbirana mkazi

Nyamata wazaka 19 ku Chilipa m’boma la Mangochi ali m’manja mwa apolisi kaamba koti akuganizilidwa kuti wapha mzake chifukwa cholimbirana mkazi. Woganiziridwayu yemwe dzina lake ndi Anusa Sausande adabaya ndikupha Kassim wazaka 21 zakubadwa pomwe adali kulimbirana mkazi. Nkhani yonse ikuti Sauzande ndiyemwe adayamba kupalana ubwezi ndi mkaziyu ndipo pakutha pa nthawi ubweziwu udatha. Apa […]

The post Nyamata wazaka 19 wapha mzake polimbirana mkazi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください