Mtsogoleri wa chipani cha DPP Peter Mutharika wati ali ndi mau omwe akufuna kumuuza mtsogoleri wa dziko lino yemweso ndi mtsogoleri wa chipani cha MCP Lazarus Chakwera lachitatu likudzali. Mutharika wayankhula izi kudzera kwa mneneri wake Shadrick Namalomba. Poyankhula ndi atolankhani mdziko muno lero, Namalomba wati Mutharika ali ndi mau omwe akufuna kuuza Chakwera pa […]
The post A Mutharika akuti ali ndi mawu oti awawuza a Chakwera, atero a Namalomba appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.