Amai ena anagwililiridwa pa ziwawa za dzulo, atero a Navicha

Mtsogoleri otsutsa boma mu nyumba ya malamulo yemwenso ndi mkulu wa amai mu chipani cha DPP, Mai Mary Navicha, wati amai ambiri apangidwa chipongwe powagwirira pa chipolowe chomwe  chinali dzulo mu mzinda  wa Lilongwe. Dzulo chipanichi chinali ndi ndawala yomeneza anthu kuti akalembetse cha unzika pokozekera chisankho cha 2025 koma anthu ena anabwera ndikukhapa anthu […]

The post Amai ena anagwililiridwa pa ziwawa za dzulo, atero a Navicha appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください