Boma kudzera ku ndondomeko ya za chuma cha dziko lino ya chaka cha 2024/2025 laika ndalama zoyambilaso ntchito yomanga bwalo la zamasewero a matimu a FCB Nyasa Big Bullets komanso Mighty Mukuru wanderers. Ntchitoyi inaima miyezi nkhumi ndi iwiri yapita kamba kosowa ndalama. Malinga ndi ndondomeko ya za chuma yomwe unduna wa za chuma watulutsa, […]
The post Boma lati ntchito yomanga mabwalo a Bullets ndi Wanderers iyambilaso appeared first on Malawi 24.