Boma kudzera ku Nthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi (DoDMA) tsopano layamba ntchito yogawa ufa ku maanja omwe akhudzidwa ndi njala m’dziko muno pansi pa ndondomeko ya Lean Season Response. Malingana ndi DoDMA, ntchitoyi yakhazikitsidwa pa 24 February, 2024 ndipo ufa wu ndi wokwana matani 23,000. M’mawu awo, nduna Yoona Zofalitsa Nkhani a Moses Kunkuyu […]
The post Boma lati layamba ntchito yogawa ufa ku maanja okhudzidwa ndi njala appeared first on Malawi 24.