Nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo m’dziko muno ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) yati kumwamba kudakali madzi amvula ochuluka kotero mvula yamabingu ikhala ikugwa m’madera ochuluka mdziko muno kufikira lachiwiri. “Agulu mmwambamu ndiye madzi alimo ndipo atsakamukamo ndithu mokuti Lero ikuonekanso yamabingu, mawanso same same, Monday nso ndithu Lachiwiri nso, […]
The post M’mwambamu ndiye madzi alimo ndipo atsakamukamo ndithu — atero a zanyengo appeared first on Malawi 24.