Kuwonjezera kwa ndalama zachitukuko za Constituency Development Fund (CDF) kuchoka pa 100 miliyoni kufika pa 200 million kwacha kunadzetsa chimwemwe chochuluka kwa aphungu ambili pamene nduna ya za chuma a Simplex Chithyola Banda anawuza nyumba ya malamulo zankhaniyi dzulo. Aphungu ena ati kukweza kwa ndalamayi kuthandiza kuti aphungu akwanilitse kutumikira anthu m’madera awo pantchito zachitukuko […]
The post Boma lawonjezera ndalama yopita kuthumba la CDF kufikapa 200 miliyoni appeared first on Malawi 24.